Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munawapatsanso maufumu, ndi mitundu ya anthu, nimunawagawa m'madera, motero analandira likhale lao lao dziko la Sihoni, ndilo dziko la mfumu ya ku Hesiboni, ndi dziko la Ogi mfumu ya ku Basana.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:22 nkhani