Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi mkate wocokera m'mwamba munawapatsa pa njala yao; ndi madzi oturuka m'thanthwe munawaturutsira pa ludzu lao, ndi kuwauza alowe, nalandire dziko limene mudakwezapo dzanja lanu kuwapatsa.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:15 nkhani