Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nimunacitira zizindikilo ndi zodabwiza Farao ndi akapolo ace onse, ndi anthu onse a m'dziko lace; popeza munadziwa kuti anawacitira modzikuza; ndipo munadzibukitsira dzina monga lero lino.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:10 nkhani