Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 8:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Yesuwa, ndi Bani, ndi Serebiya, Yamini, Akubu, Sabetai, Hodayi, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi, Hanani, Pelaya, ndi Alevi, anadziwitsa anthu cilamuloco; ndi anthu anali ciriri pamalo pao,

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8

Onani Nehemiya 8:7 nkhani