Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 7:73 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nakhala m'midzi mwao ansembe, ndi Alevi, ndi odikira, ndi oyimbira, ndi anthu ena, ndi Anetini, ndi Aisrayeli onse.Utakhala tsono mwezi wacisanu ndi ciwiri ana a Israyeli anakhala m'midzi mwao.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:73 nkhani