Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 7:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Odikira: ana a Salumu, ana a Ateri, ana a Talimoni, ana a Akubu, ana a Hatita, ana a Sobai, zana limodzi mphambu makumi atatu kudza asanu ndi atatu.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:45 nkhani