Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 7:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinanenanso nao, Asatsegule pa zipata za Yerusalemu lisanafunde dzuwa; ndi poimirira odikira atseke pazipata, nimuzipiringidze, nimuike alonda mwa iwo okhala m'Yerusalemu, yense polindirira pace, yense pandunji pa nyumba yace.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:3 nkhani