Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ambiri m'Yuda analumbirirana naye cibwenzi; popeza ndiye mkamwini wace wa Sekaniya mwana wa Ara; ndi mwana wace Yehohanana adadzitengera mwana wamkazi wa Mesulamu mwana wa Berekiya.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 6

Onani Nehemiya 6:18 nkhani