Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinalowa m'nyumba ya Semaya mwana wa Delaya, mwana wa Mehetabele, wobindikizidwayo, ndipo anati, Tikomane ku nyumba ya Mulungu m'kati mwa Kacisi, titsekenso pa makomo a Kacisi; pakuti akudza kudzapha iwe, inde akudza usiku kudzapha iwe.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 6

Onani Nehemiya 6:10 nkhani