Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 5:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano thupi lathu likunga thupi la abale athu, ana athu akunga ana ao; ndipo taonani, titengetsa ana athu amuna ndi akazi akhale akapolo, ndi ana athu akazi ena tawatengetsa kale; ndipo tiribe ife mphamvu ya kucitapo kanthu; ndi minda yathu, ndi minda yathu yampesa, nja ena.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 5

Onani Nehemiya 5:5 nkhani