Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 5:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zokonzekeratu tsiku limodzi tsono ndizo ng'ombe imodzi, ndi nkhosa zonenepa zisanu ndi imodzi, anandikonzeratunso nkhuku, ndi kamodzi atapita masiku khumi vinyo wambiri wa mitundu mitundu; cinkana conseci sindinafunsira cakudya ca kazembe, popeza ukapolo unalemerera anthuwo.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 5

Onani Nehemiya 5:18 nkhani