Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi omanga linga ali yense anamangirira lupanga lace m'cuuno mwace, nagwira nchito motero. Ndipo woomba lipenga anali ndi ine.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 4

Onani Nehemiya 4:18 nkhani