Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pambali pace anakonza Uziyeli mwana wa Haraya, wa iwo osula golidi. Ndi padzanja pace anakonza Hananiya, wa iwo osanganiza zonunkhira; nalimbikitsa Yerusalemu mpaka linga lacitando.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3

Onani Nehemiya 3:8 nkhani