Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 3:27-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Potsatizana nao Atekoa anakonza gawo lina, pandunji pa nsanja yaikuru yosomphoka ndi ku linga la Ofeli.

28. Kumtunda kwa cipata ca akavalo anakonza ansembe, yense pandunji pa nyumba yace.

29. Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yace. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga cipata ca kum'mawa.

30. Potsatizana naye Hananiya mwana wa Selemiya, ndi Hanuni mwana wacisanu ndi cimodzi wa Salafi, anakonza gawo lina. Potsatizana naye anakonza Mesulamu mwana wa Berekiya pandunji pa cipinda cace.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3