Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Eliasibu mkuru wa ansembe ananyamuka pamodzi ndi abale ace ansembe, namanga cipata cankhosa; anacipatula, naika zitseko zace, inde anacipatula mpaka nsanja ya Mea, mpaka nsanja ya Hananeeli.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3

Onani Nehemiya 3:1 nkhani