Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinafika tsono kwa ziwanga za tsidya lino la mtsinje, ndipo ndinawapatsa akalata a mfumu. Koma mfumu idatumiza apite nane akazembe a nkhondo, ndi apakavalo.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 2

Onani Nehemiya 2:9 nkhani