Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pocitika ici conse sindinakhala ku Yerusalemu; pakuti caka ca makumi atatu ndi caciwiri ca Aritasasta mfumu ya Babulo ndinafika kwa mfumu, ndipo atapita masiku ena ndinapempha mfumu indilole;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13

Onani Nehemiya 13:6 nkhani