Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 13:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Momwemo ndinawayeretsa kuwacotsera acilendo onse, ndi kuikira udikiro ansembe ndi Alevi, yense ku nchito yace;

31. ndi copereka ca nkhuni pa nthawi zoikika, ndi wa zipatso zoyamba. Mundikumbukile, Mulungu wanga, cindikomere.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13