Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 13:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinatsutsana nao, ndi kuwatemberera, ndi kukantha ena a iwo, ndi kumwetula tsitsi lao, ndi kuwalumbiritsa pa Mulungu ndi kuti, Musapereka ana anu akazi kwa ana ao amuna, kapena kutengera ana anu amuna, kapena a inu nokha, ana ao akazi.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13

Onani Nehemiya 13:25 nkhani