Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 13:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, kukadayamba cizirezire pa zipata za Yerusalemu, losafika Sabata, ndinawauza atseke pamakomo; ndinawauzanso kuti asatsegulepo, koma litapita Sabata ndipo; ndipo ndinaimika anyamata anga ena pazipata, kuti pasalowe katundu dzuwa la Sabata.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13

Onani Nehemiya 13:19 nkhani