Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 13:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinaikanso osunga cuma, asunge nyumba za cuma: Selemiya wansembe, ndi Zadoki mlembi; ndi wa Alevi, Pedaya; ndi wakuwathandiza, Hanani mwana wa Zakuri, mwana wa Mataniya; popeza anayesedwa okhulupirika ndi udindo wao, ndiwo kugawira abale ao.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 13

Onani Nehemiya 13:13 nkhani