Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 12:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi gulu lina la oyamikira linamuka mokomana nao, ndi ine ndinawatsata, pamodzi ndi limodzi la magawo awiri la anthu palinga, napitirira pa nsanja ya ng'anjo, mpaka ku linga lacitando;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12

Onani Nehemiya 12:38 nkhani