Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 12:1-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ansembe ndi Alevi amene anakwera ndi Zerubabele mwana wa Sealtiyeli, ndi Yesuwa, ndi awa: Seraya, Yeremiya, Ezara,

2. Amariya, Maluki, Hatusi,

3. Sekaniya, Rehumu, Meremoti,

4. Ido, Ginetoi, Abiya,

5. Miyamini, Maadiya, Biliga,

6. Semaya, ndi Yoyaribi, Yedaya,

7. Salu, Amoki, Hilikiya, Yedaya. Awa ndi akuru a ansembe ndi abale ao m'masiku a Yesuwa.

8. Ndi Alevi ndiwo Yesuwa, Binui, Kadimiyeli, Serebiya, Yuda, ndi Mataniya; iye ndi abale ace amatsogolera mayamiko.

9. Ndi Bakibukiya ndi Uni, abale ao, anawayang'anira maulonda.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12