Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 12:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ansembe ndi Alevi amene anakwera ndi Zerubabele mwana wa Sealtiyeli, ndi Yesuwa, ndi awa: Seraya, Yeremiya, Ezara,

2. Amariya, Maluki, Hatusi,

3. Sekaniya, Rehumu, Meremoti,

4. Ido, Ginetoi, Abiya,

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12