Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 11:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo woyang'anira wa Alevi m'Yerusalemu ndiye Uzi mwana wa Bani, mwana wa Hasabiya, mwana wa Mataniya, mwana wa Mika; mwa ana a Asafu oyimbira ena anayang'anira nchito ya m'nyumba ya Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11

Onani Nehemiya 11:22 nkhani