Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi Mataniya mwana wa Mika, mwana wa Zabidi, mwana wa Asafu, ndiye mkuru wakuyamba mayamiko, popemphera; ndi Bakibukiya wotsatana naye mwa abale ace, ndi Abida mwana wa Samua, mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11

Onani Nehemiya 11:17 nkhani