Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 11:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi abale ao ocita nchito ya m'nyumbayi ndiwo mazana asanu ndi atatu mphambu makumi awiri kudza awiri; ndi Adaya mwana wa Yerohamu, mwana wa Pelaliya, mwana wa Amzi, mwana wa Zekariya, mwana: wa Pasuru, mwana wa Malikiya;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11

Onani Nehemiya 11:12 nkhani