Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuru anthu anakhala m'Yerusalemu; anthu otsala omwe anacita maere, kuti libwere limodzi la magawo khumi likhale m'Yerusalemu, mudzi wopatulika, ndi asanu ndi anai a khumi m'midzi yina.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 11

Onani Nehemiya 11:1 nkhani