Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 10:1-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Okomera cizindikilo tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya,

2. Seraya, Agariya, Yeremiya,

3. Pasuri, Amariya, Malikiya,

4. Hatusi, Sebaniya, Maluki,

5. Harimu, Meremoti, Obadiya,

6. Danieli, Ginetoni, Baruki,

7. Mesulamu, Abiya, Miyamini,

8. Maaziya, Biligai, Semaya, ndiwo ansembe.

9. Ndi Alevi ndiwo Yesuwa mwana wa Azaniya, Binui wa ana a Henadadi, Kadiniyeli;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 10