Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 10:1-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Okomera cizindikilo tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya,

2. Seraya, Agariya, Yeremiya,

3. Pasuri, Amariya, Malikiya,

4. Hatusi, Sebaniya, Maluki,

5. Harimu, Meremoti, Obadiya,

6. Danieli, Ginetoni, Baruki,

7. Mesulamu, Abiya, Miyamini,

8. Maaziya, Biligai, Semaya, ndiwo ansembe.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 10