Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma mukabwerera kudza kwa Ine, ndi kusunga malamulo anga, ndi kuwacita, angakhale otayika anu anali ku malekezero a thambo, ndidzawasonkhanitsa kucokera komweko, ndi kubwera nao ku malo ndinawasankha kukhalitsako dzina langa.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 1

Onani Nehemiya 1:9 nkhani