Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nahumu 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Obvala korona ako akunga dzombe, ndi akazembe, ndi akazembe ako ngati ziwalamsatsi zakutera m'macinga tsiku lacisanu, koma likafundukula dzuwa ziuluka nizithawa, ndi kumene zinakhalako sikudziwikanso.

Werengani mutu wathunthu Nahumu 3

Onani Nahumu 3:17 nkhani