Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nahumu 3:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye anatengedwa, analowa ndende; ana ace a makanda anaphwanyika polekeza pace pa miseu yace yonse; ndi pa omveka ace anacita maere, ndi akulu ace onse anamangidwa maunyolo.

Werengani mutu wathunthu Nahumu 3

Onani Nahumu 3:10 nkhani