Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nahumu 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zikopa za amphamvu ace zasanduka zofiira, ngwazi zibvala mlangali; magareta anyezimira ndi citsulo tsiku la kukonzera kwace, ndi mikondo itinthidwa.

Werengani mutu wathunthu Nahumu 2

Onani Nahumu 2:3 nkhani