Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nahumu 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani pamapiri mapazi a iye wakulalikira uthenga wabwino, wakubukitsa mtendere! cita madyerero ako, Yuda, kwaniritsa zowinda zako; pakuti wopanda paceyo sadzapitanso mwa iwe; iye waonongeka konse.

Werengani mutu wathunthu Nahumu 1

Onani Nahumu 1:15 nkhani