Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 9:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Mau a anzeru acete amveka koposa kupfuula kwa wolamulira mwa zitsiru.

18. Nzeru ipambana zida za nkhondo; koma wocimwa mmodzi aononga zabwino zambiri.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 9