Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 8:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pompo ndinapereka mtima wanga kudziwa nzeru, ndi kupenya nchito zicitidwa pansi pano; kuti anthu saona tulo konse ndi maso ao ngakhale usana ngakhale usiku;

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 8

Onani Mlaliki 8:16 nkhani