Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 8:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pali cinthu cacabe cimacitidwa pansi pano; cakuti alipo olungama amene aona zomwe ziyenera nchito za oipa, ndipo alipo oipa amene aona zomwe ziyenera nchito za olungama, Ndinati, Icinso ndi cabe.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 8

Onani Mlaliki 8:14 nkhani