Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 8:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndani akunga wanzeru? Ndani adziwa tanthauzo la mau? Nzeru ya munthu iwalitsa nkhope yace, kuduwa kwa nkhope yace ndi kusanduka.

2. Nditi, Sunga mau a mfumu, makamaka m'kulumbira Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 8