Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 7:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndinapeza kanthu kowawa koposa imfa, ndiko mkazi amene ndiye msampha, mtima wace ukunga maukonde, manja ace ndiwo matangadza; yemwe Mulungu amuyesa wabwino adzapulumuka kwa iye; koma wocimwa adzagwidwa naye.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 7

Onani Mlaliki 7:26 nkhani