Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usalankhule mwanthuku mtima wako, usafulumire kunena kanthu pamaso pa Mulungu; pakuti Mulungu ali kumwamba, iwe uli pansi; cifukwa cace mau ako akhale owerengeka.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5

Onani Mlaliki 5:2 nkhani