Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 5:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Inde yemwe Mulungu wamlemeretsa nampatsa cuma, namninkhanso mphamvu ya kudyapo, ndi kulandira gawo lace ndi kukondwera ndi nchito zace; umenewu ndiwo mtulo wa Mulungu.

20. Pakuti sadzakumbukira masiku a moyo wace kwambiri; cifukwa Mulungu ambvomereza m'cimwemwe ca mtima wace.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5