Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tulo ta munthu wogwira nchito ntabwino, ngakhale adya pang'ono ngakhale zambiri; koma kukhuta kwa wolemera sikumgonetsa tulo.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 5

Onani Mlaliki 5:12 nkhani