Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 3:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti comwe cigwera ana a anthu cigweranso nyamazo; ngakhale cowagwera ncimodzimodzi; monga winayo angofa momwemo zinazo zifanso; inde onsewo ali ndi mpweya umodzi; ndipo munthu sapambana nyama pakuti zonse ndi cabe,

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 3

Onani Mlaliki 3:19 nkhani