Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinati mumtima wanga, Mulungu adzaweruza wolungama ndi woipa; pakuti pamenepo pali mphindi ya zofuna zonse ndi nchito zonse.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 3

Onani Mlaliki 3:17 nkhani