Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndinakundikanso siliva ndi golidi ndi cuma ca mafumu ndi madera a dziko; ndinaitanitsa amuna ndi akazi akuyimba ndi zokondweretsazo za ana a anthu, ndizo zoyimbira za mitundu mitundu.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2

Onani Mlaliki 2:8 nkhani