Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wanzeru maso ace ali m'mutu wace, koma citsiru ciyenda mumdima; ndipo nanenso ndinazindikira kuti comwe ciwagwera onsewo ndi cimodzi.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2

Onani Mlaliki 2:14 nkhani