Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 12:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

inde, adzaopa za pamwamba, panjira padzakhala zoopsya; mciu nudzaphuka, dzombe ndi kukoka miyendo, zilakolako ndi kutha; pakuti munthu apita kwao kwamuyaya, akulira maliro nayendayenda panja;

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 12

Onani Mlaliki 12:5 nkhani