Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 12:13-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Mau atha; zonse zamveka zatha; opa Mulungu, musunge malamulo ace; pakuti coyenera anthu onse ndi ici.

14. Pakuti Mulungu adzanena mlandu wa zocita zonse, ndi zobisika zonse, ngakhale zabwino ngakhale zoipa.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 12