Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 10:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Wosendeza miyala adzaphwetekedwa nayo; wowaza nkhuni nadzitema.

10. Citsulo cikakhala cosathwa, ndipo ukaleka kunola, uzipambana kulimbikira; koma nzeru ipindulira pocenjeza.

11. Njoka ikaluma isanalodzedwe, watsenga saona mphotho.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 10